Marko 1:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo m'mawa mwake anauka usikusiku, natuluka namuka kuchipululu, napemphera kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo m'mawa mwake anauka usikusiku, natuluka namuka kuchipululu, napemphera kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 M'mamaŵa ndithu, kusanache, Yesu adadzuka napita kumalo kosapitapita anthu. Kumeneko adakapemphera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Mmamawa, kukanali kamdima, Yesu anadzuka, nachoka pa nyumbapo kupita kumalo kwa yekha, kumene anakapemphera. Onani mutuwo |