Marko 1:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo madzulo, litalowa dzuwa, anadza nao kwa Iye onse akudwala, ndi akugwidwa ndi ziwanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo madzulo, litalowa dzuwa, anadza nao kwa Iye onse akudwala, ndi akugwidwa ndi ziwanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Madzulo amenewo, dzuŵa litaloŵa, anthu adabwera kwa Yesu ndi anzao onse ovutika, ndi ogwidwa ndi mizimu yoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Madzulo omwewo dzuwa litalowa anthu anabweretsa kwa Yesu anthu onse odwala ndi ogwidwa ndi ziwanda. Onani mutuwo |