Marko 1:31 - Buku Lopatulika31 ndipo anadza namgwira dzanja, namuutsa; ndipo malungo anamleka, ndipo anawatumikira iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 ndipo anadza namgwira dzanja, namuutsa; ndipo malungo anamleka, ndipo anawatumikira iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Yesu adapita nakaŵagwira pa dzanja amaiwo nkuŵadzutsa, ndipo malungowo adatha. Pomwepo amai aja adayamba kukonzera anthu chakudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Ndipo Yesu anapita kwa iye, namugwira dzanja namuthandiza kudzuka. Malungo anachoka ndipo anayamba kuwatumikira. Onani mutuwo |