Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 1:29 - Buku Lopatulika

29 Ndipo pomwepo, potuluka m'sunagoge, iwo analowa m'nyumba ya Simoni ndi Andrea pamodzi ndi Yakobo ndi Yohane.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Ndipo pomwepo, potuluka m'sunagoge, iwo analowa m'nyumba ya Simoni ndi Andrea pamodzi ndi Yakobo ndi Yohane.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Pambuyo pake Yesu adachoka ku nyumba yamapemphero kuja, nakaloŵa pamodzi ndi Yakobe ndi Yohane m'nyumba ya Simoni ndi Andrea.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Atangochoka mu sunagoge, Yesu pamodzi ndi Yakobo ndi Yohane anakalowa mʼnyumba ya Simoni ndi Andreya.

Onani mutuwo Koperani




Marko 1:29
7 Mawu Ofanana  

Ndipo iwo analowa mu Kapernao; ndipo pomwepo pa tsiku la Sabata iye analowa m'sunagoge naphunzitsa.


Ndipo pomwepo panali munthu m'sunagoge mwao ali ndi mzimu wonyansa; ndipo anafuula iye.


Ndipo mbiri yake inabuka pompaja kudziko lonse la Galileya lozungulirapo.


Ndipo mpongozi wake wa Simoni anali gone wodwala malungo; ndipo pomwepo anamuuza za iye:


Ndipo Yesu anati kwa iye, Nkhandwe zili nazo nkhwimba, ndi mbalame za kumwamba zisa, koma Mwana wa Munthu alibe potsamira mutu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa