Marko 1:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anazizwa ndi chiphunzitso chake; pakuti anaphunzitsa monga mwini mphamvu, si monga alembi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anazizwa ndi chiphunzitso chake; pakuti anaphunzitsa monga mwini mphamvu, si monga alembi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Zophunzitsa zake anthu zidaaŵagwira mtima kwambiri, chifukwa ankaphunzitsa moonetsa ulamuliro, kusiyana ndi m'mene ankachitira aphunzitsi a Malamulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Anthu anadabwa ndi chiphunzitso chake, chifukwa anawaphunzitsa ngati munthu amene anali ndi ulamuliro, osati ngati aphunzitsi amalamulo. Onani mutuwo |