Marko 1:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo iwo analowa mu Kapernao; ndipo pomwepo pa tsiku la Sabata iye analowa m'sunagoge naphunzitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo iwo analowa m'Kapernao; ndipo pomwepo pa tsiku la Sabata iye analowa m'sunagoge naphunzitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Onsewo adapita ku Kapernao. Tsono litafika tsiku la Sabata, Yesu adaloŵa m'nyumba yamapemphero, nayamba kuphunzitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Iwo anapita ku Kaperenawo, ndipo tsiku la Sabata litafika, Yesu analowa mʼsunagoge nayamba kuphunzitsa. Onani mutuwo |