Marko 1:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo pomwepo panali munthu m'sunagoge mwao ali ndi mzimu wonyansa; ndipo anafuula iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo pomwepo panali munthu m'sunagoge mwao ali ndi mzimu wonyansa; ndipo anafuula iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 M'nyumba yamapempheroyo mudaaloŵa munthu wogwidwa ndi mzimu womuipitsa. Adalankhula mokuŵa kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pomwepo munthu wina mʼsunagogemo amene anali wogwidwa ndi mzimu woyipa anafuwula kuti, Onani mutuwo |