Marko 1:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo pomwepo, alimkukwera potuluka m'madzi, anaona Iye thambo litang'ambika, ndi Mzimu alikutsikira pa Iye monga nkhunda: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo pomwepo, alimkukwera potuluka m'madzi, anaona Iye thambo litang'ambika, ndi Mzimu alikutsikira pa Iye monga nkhunda: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Potuluka m'madzimo, adangoona kuthambo kukutsekuka, ndipo Mzimu Woyera akutsika pa Iye ngati nkhunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pamene Yesu ankatuluka mʼmadzi, anaona kumwamba kukutsekuka ndipo Mzimu Woyera akutsikira pa Iye ngati nkhunda. Onani mutuwo |