Marko 1:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo kunali masiku omwewo, Yesu anadza kuchokera ku Nazarete wa ku Galileya, nabatizidwa ndi Yohane mu Yordani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo kunali masiku omwewo, Yesu anadza kuchokera ku Nazarete wa ku Galileya, nabatizidwa ndi Yohane m'Yordani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pa masiku amenewo Yesu adafika kuchokera ku Nazarete, mudzi wa ku Galileya, ndipo Yohane adambatiza mu mtsinje wa Yordani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pa nthawi imeneyo Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu mtsinje wa Yorodani. Onani mutuwo |