Marko 1:11 - Buku Lopatulika11 ndipo mau anatuluka m'thambo, Mwana wanga wokondedwa ndiwe, mwa Iwe ndikondwera bwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndipo mau anatuluka m'thambo, Mwana wanga wokondedwa ndiwe, mwa Iwe ndikondwera bwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono kudamveka mau ochokera kumwamba akuti, “Iwe ndiwe Mwana wanga wapamtima. Ndimakondwera nawe kwambiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ndipo Mawu anamveka kuchokera kumwamba: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa; ndipo ndikondwera nawe.” Onani mutuwo |