Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Maliro 5:3 - Buku Lopatulika

3 Ndife amasiye opanda atate, amai athu akunga akazi amasiye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndife amasiye opanda atate, amai athu akunga akazi amasiye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ife tili ngati ana amasiye, opanda bambo wao. Amai athu ali ngati akazi amasiye.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Takhala amasiye ndi wopanda abambo, amayi athu ali ngati akazi amasiye.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 5:3
5 Mawu Ofanana  

Ukawazunza ndi kakuti konse, nakandilirira pang'ono ponse iwowa, ndidzamvadi kulira kwao;


ndi mkwiyo wanga udzayaka, ndipo ndidzapha inu ndi lupanga; ndipo akazi anu adzakhala amasiye, ndi ana anu omwe.


Amasiye ao andichulukira Ine kopambana mchenga wa kunyanja; ndatengera wofunkha usana afunkhire mai wao wa anyamata; ndamgwetsera dzidzidzi kuwawa mtima ndi mantha.


Chifukwa chake mupereke ana ao kunjala, mupereke iwo kumphamvu ya lupanga; akazi ao akhale opanda ana, ndi amasiye; amuna ao aphedwe ndi imfa, ndi anyamata ao apandidwe ndi lupanga kunkhondo.


Asiriya sadzatipulumutsa; sitidzayenda pa akavalo, ndipo sitidzanenanso kwa ntchito ya manja athu, Inu ndinu milungu yathu; pakuti mwa Inu ana amasiye apeza chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa