Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Maliro 5:4 - Buku Lopatulika

4 Tinamwa madzi athu ndi ndalama, tiona nkhuni zathu pozigula.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Tinamwa madzi athu ndi ndalama, tiona nkhuni zathu pozigula.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Madzi amene timamwaŵa tiyenera kuchita chogula. Nkhuni zosonkhera moto nzoyeneranso kuchita chogula.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Tiyenera kugula madzi amene timamwa, nkhuni zathunso nʼzogula.

Onani mutuwo Koperani




Maliro 5:4
5 Mawu Ofanana  

Tapenyani, ife lero ndife akapolo, ndi dzikoli mudalipereka kwa makolo athu kudya zipatso zake ndi zokoma zake, taonani, ife ndife akapolo m'menemo.


Ndipo onani, Ambuye, Yehova wa makamu, wachotsa ku Yerusalemu ndi ku Yuda mchirikizo wochirikiza chakudya chonse ndi madzi onse, zimene zinali mchirikizo;


Inu nonse, inu akumva ludzu, idzani kumadzi; ndi osowa ndalama idzani inu mugule mudye; inde idzani, mugule vinyo ndi mkaka opanda ndalama ndi opanda mtengo wake.


chifukwa chake mudzatumikira adani anu amene Yehova adzakutumizirani, ndi njala, ndi ludzu, ndi usiwa, ndi kusowa zinthu zonse; ndipo adzaika goli lachitsulo pakhosi panu, kufikira atakuonongani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa