Malaki 1:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo maso anu adzaona, nimudzati, Yehova ali wamkulu kupitirira malire a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo maso anu adzaona, nimudzati, Yehova ali wamkulu kupitirira malire a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Inu, Aisraele, mudzaziwona zimenezi ndi maso anu. Inu nomwe mudzati, “Ukulu wa Chauta umafika ngakhale kunja kwa malire a Aisraele.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Inu mudzaziona zimenezi ndi maso anu ndipo mudzati, ‘Yehova ndi Wamkulu, ukulu wake umafika ngakhale kunja kwa malire a Israeli!’ Onani mutuwo |