Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 9:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo amunawo akumperekeza iye anaima duu, atamvadi mau, koma osaona munthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo amunawo akumperekeza iye anaima duu, atamvadi mau, koma osaona munthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Anthu amene anali naye pa ulendowo adaima, atangoti chete. Mauwo ankaŵamva, koma osaona munthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Anthu amene anali naye paulendo, anasowa chonena; iwo anamva mawu koma sanaone wina aliyense.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 9:7
5 Mawu Ofanana  

Ndipo ine Daniele ndekha ndinaona masomphenyawo; pakuti anthu anali nane sanaone masomphenyawo; koma kunawagwera kunjenjemera kwakukulu, nathawa kubisala.


Chifukwa chake khamu la anthu akuimirirako, ndi kuwamva ananena kuti kwagunda. Ena ananena, Mngelo walankhula ndi Iye.


Ndipo iwo akukhala nane anaonadi kuunika, koma sanamve mau akulankhula nane.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa