Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 9:12 - Buku Lopatulika

12 ndipo anaona mwamuna dzina lake Ananiya, alikulowa, namuika manja, kuti apenyenso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 ndipo anaona mwamuna dzina lake Ananiya, alikulowa, namuika manja, kuti apenyenso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 ndipo waona m'masomphenya munthu wina, dzina lake Ananiya, akuloŵa ndi kumsanjika manja kuti apenyenso.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ndipo waona mʼmasomphenya munthu, dzina lake Hananiya atabwera ndi kumusanjika manja kuti aonenso.”

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 9:12
4 Mawu Ofanana  

nanena, kuti, Kamwana kanga kabuthu kalinkutsirizika; ndikupemphani Inu mufikeko, muike manja anu pa iko, kuti kapulumuke, ndi kukhala ndi moyo.


amenewo anawaika pamaso pa atumwi; ndipo m'mene adapemphera, anaika manja pa iwo.


Koma ku Damasiko kunali wophunzira wina dzina lake Ananiya; ndipo Ambuye anati kwa iye m'masomphenya, Ananiya. Ndipo anati, Ndili pano, Ambuye,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa