Machitidwe a Atumwi 9:1 - Buku Lopatulika1 Koma Saulo, wosaleka kupumira pa ophunzira a Ambuye kuopsa ndi kupha, ananka kwa mkulu wa ansembe, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma Saulo, wosaleka kupumira pa ophunzira a Ambuye kuopsa ndi kupha, ananka kwa mkulu wa ansembe, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Saulo uja ankaopsezabe ophunzira a Ambuye, nkumafuna kuŵapha. Adapita kwa mkulu wa ansembe onse Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pa nthawi imeneyi, Saulo ankaopsezabe okhulupirira Ambuye nafuna kuwapha. Iye anapita kwa mkulu wa ansembe, Onani mutuwo |