Machitidwe a Atumwi 7:53 - Buku Lopatulika53 inu amene munalandira chilamulo monga chidaikidwa ndi angelo, ndipo simunachisunge. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 inu amene munalandira chilamulo monga chidaikidwa ndi angelo, ndipo simunachisunga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Inu mudaalandira Malamulo a Mulungu kudzera mwa angelo, komabe simudaŵasunge konse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Inu amene munalandira Malamulo amene anaperekedwa ndi angelo ndipo simunawamvere.” Onani mutuwo |