Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 7:20 - Buku Lopatulika

20 Nyengo yomweyo anabadwa Mose, ndiye wokoma ndithu pamaso pa Mulungu; ndipo anamlera miyezi itatu m'nyumba ya atate wake:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Nyengo yomweyo anabadwa Mose, ndiye wokoma ndithu pamaso pa Mulungu; ndipo anamlera miyezi itatu m'nyumba ya atate wake:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Nthaŵi imeneyo Mose adabadwa, ndipo anali mwana wokongola kwambiri. Adamlera kwao miyezi itatu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 “Pa nthawi imeneyo Mose anabadwa, ndipo anali wokongola kwambiri. Iye analeredwa mʼnyumba ya abambo ake kwa miyezi itatu.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 7:20
3 Mawu Ofanana  

Ndi chikhulupiriro Mose, pobadwa, anabisidwa miyezi itatu ndi akum'bala, popeza anaona kuti ali mwana wokongola; ndipo sanaope chilamuliro cha mfumu.


Ndipo anatumiza munthu, nabwera naye. Tsono iye anali wofiirira, ndi wa nkhope yokongola, ndi maonekedwe okoma. Ndipo Yehova anati, Nyamuka umdzoze, pakuti ndi ameneyu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa