Machitidwe a Atumwi 7:19 - Buku Lopatulika19 Imeneyo inachenjerera fuko lathu, niwachitira choipa makolo athu, niwatayitsa tiana tao, kuti tingakhale ndi moyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Imeneyo inachenjerera fuko lathu, niwachitira choipa makolo athu, niwatayitsa tiana tao, kuti tingakhale ndi moyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mfumuyo idachenjerera mtundu wathu, nkuyamba kuzunza makolo athu, pakuŵatayitsa ana ao akhanda kuti asakhale ndi moyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mfumuyo inachita mwachinyengo ndi mtundu wathu ndi kuwazunza kuti ataye ana awo akhanda kuti afe. Onani mutuwo |