Machitidwe a Atumwi 7:21 - Buku Lopatulika21 ndipo pakutayika iye, anamtola mwana wamkazi wa Farao, namlera akhale mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 ndipo pakutayika iye, anamtola mwana wamkazi wa Farao, namlera akhale mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 koma atamsiya pamtsinje paja, mwana wamkazi wa Farao adamtola, namlera ngati mwana wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Atakamutaya, mwana wamkazi wa Farao anamutola nakamulera ngati mwana wake. Onani mutuwo |