Machitidwe a Atumwi 7:18 - Buku Lopatulika18 kufikira inauka mfumu ina pa Ejipito, imene siinamdziwe Yosefe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 kufikira inauka mfumu ina pa Ejipito, imene siinamdziwa Yosefe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pambuyo pake mfumu ina imene sidadziŵe Yosefe, idayamba kulamulira ku Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pambuyo pake mfumu yatsopano imene sinkamudziwa Yosefe, inayamba kulamulira dziko la Igupto. Onani mutuwo |