Machitidwe a Atumwi 7:17 - Buku Lopatulika17 Koma m'mene inayandikira nthawi ya lonjezo limene Mulungu adalonjezana ndi Abrahamu, anthuwo anakula nachuluka mu Ejipito, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma m'mene inayandikira nthawi ya lonjezo limene Mulungu adalonjezana ndi Abrahamu, anthuwo anakula nachuluka m'Ejipito, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 “Pamene idayandikira nthaŵi yakuti Mulungu achite zimene adaalonjeza kwa Abrahamu, mtundu wathu udakula ndi kuchuluka ku Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 “Nthawi itayandikira yakuti Mulungu achite zimene analonjeza kwa Abrahamu, mtundu wathu unakula ndi kuchuluka kwambiri mu Igupto. Onani mutuwo |