Machitidwe a Atumwi 5:2 - Buku Lopatulika2 anagulitsa chao, napatula pa mtengo wake, mkazi yemwe anadziwa, natenga chotsala, nachiika pa mapazi a atumwi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 anagulitsa chao, napatula pa mtengo wake, mkazi yemwe anadziwa, natenga chotsala, nachiika pa mapazi a atumwi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mopangana ndi mkazi wake, adapatulapo ndalama zina za mundawo, nakapereka zotsala kwa atumwi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mogwirizana ndi mkazi wakeyo anapatulapo pa ndalamazo nazisunga, ndipo anatenga zotsalazo ndi kukapereka kwa atumwi. Onani mutuwo |