Machitidwe a Atumwi 5:1 - Buku Lopatulika1 Koma munthu wina dzina lake Ananiya pamodzi ndi Safira mkazi wake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma munthu wina dzina lake Ananiya pamodzi ndi Safira mkazi wake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Munthu winanso, dzina lake Ananiya, pamodzi ndi mkazi wake Safira, adagulitsa munda wao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Koma munthu wina dzina lake Hananiya, pamodzi ndi mkazi wake Safira, anagulitsanso munda wawo. Onani mutuwo |