Machitidwe a Atumwi 4:37 - Buku Lopatulika37 pokhala nao munda, anaugulitsa, nabwera nazo ndalama zake, naziika pa mapazi a atumwi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 pokhala nao munda, anaugulitsa, nabwera nazo ndalama zake, naziika pa mapazi a atumwi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Nayenso adagulitsa munda wake, nabwera ndi ndalama zake kudzazipereka kwa atumwi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 anagulitsa munda wake ndipo anadzapereka ndalamazo kwa atumwi. Onani mutuwo |