Machitidwe a Atumwi 4:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo Petro, wodzala ndi Mzimu Woyera anati kwa iwo, Oweruza a anthu inu, ndi akulu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo Petro, wodzala ndi Mzimu Woyera anati kwa iwo, Oweruza a anthu inu, ndi akulu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Petro, atadzazidwa ndi Mzimu Woyera, adaŵayankha kuti, “Inu atsogoleri ndi akuluakulu muli apa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Petro wodzazidwa ndi Mzimu Woyera, anawawuza kuti, “Inu olamulira ndi akulu! Onani mutuwo |