Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 4:6 - Buku Lopatulika

6 ndi Anasi mkulu wa ansembe, ndi Kayafa, ndi Yohane, ndi Aleksandro, ndi onse amene anali a fuko la mkulu wa ansembe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 ndi Anasi mkulu wa ansembe, ndi Kayafa, ndi Yohane, ndi Aleksandro, ndi onse amene anali a fuko la mkulu wa ansembe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Kunalinso Anasi mkulu wa ansembe onse, pamodzi ndi Kayafa, Yohane, Aleksandro ndi ena onse a kubanja kwa mkulu wa ansembe onse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Panali Anasi, Mkulu wa ansembe, Kayafa, Yohane ndi Alekisandro ndi ana a banja la mkulu wa ansembe.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 4:6
7 Mawu Ofanana  

Pomwepo anasonkhana ansembe aakulu, ndi akulu a anthu, kubwalo la mkulu wa ansembe, dzina lake Kayafa;


pa ukulu wansembe wao wa Anasi ndi Kayafa, panadza mau a Mulungu kwa Yohane mwana wa Zekariya m'chipululu.


Koma wina mmodzi wa mwa iwo, Kayafa, wokhala mkulu wa ansembe chaka chomwecho anati kwa iwo, Simudziwa kanthu konse inu,


Koma Anasi adamtumiza Iye womangidwa kwa Kayafa mkulu wa ansembe.


Ndipo m'mene anawaimika pakati, anafunsa kuti, Ndi mphamvu yanji, kapena m'dzina lanji, mwachita ichi inu?


Ndipo atamva ichi, analowa mu Kachisi mbandakucha, naphunzitsa. Koma anadza mkulu wa ansembe ndi iwo amene anali naye, nasonkhanitsa a bwalo la akulu a milandu, ndi akulu onse a ana a Israele, natuma kundende atengedwe ajawo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa