Machitidwe a Atumwi 4:5 - Buku Lopatulika5 Koma panali m'mawa mwake, anasonkhana pamodzi mu Yerusalemu oweruza, ndi akulu, ndi alembi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Koma panali m'mawa mwake, anasonkhana pamodzi m'Yerusalemu oweruza, ndi akulu, ndi alembi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 M'maŵa mwake atsogoleri a Ayuda, akulu ao, ndiponso aphunzitsi a Malamulo adasonkhana ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mmawa mwake olamulira, akulu ndi aphunzitsi a malamulo anasonkhana mu Yerusalemu. Onani mutuwo |