Machitidwe a Atumwi 4:4 - Buku Lopatulika4 Koma ambiri a iwo amene adamva mau anakhulupirira; ndipo chiwerengero cha amuna chinali ngati zikwi zisanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma ambiri a iwo amene adamva mau anakhulupirira; ndipo chiwerengero cha amuna chinali ngati zikwi zisanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma ambiri mwa anthu amene adamva mau aja a atumwi adakhulupirira. Chiŵerengero cha okhulupirirawo chidaakwanira ngati zikwi zisanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma anthu ambiri amene anamva uthenga anakhulupirira, ndipo chiwerengero cha anthu chinakwana 5,000. Onani mutuwo |