Machitidwe a Atumwi 4:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anawathira manja, nawaika m'ndende kufikira m'mawa; pakuti mpa madzulo pamenepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anawathira manja, nawaika m'ndende kufikira m'mawa; pakuti mpa madzulo pamenepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono adaŵagwira, ndipo poti kunali kutada kale, adaŵaika m'ndende kufikira m'maŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iwo anagwira Petro ndi Yohane, popeza kunali kutada, anawayika mʼndende mpaka mmawa mwake. Onani mutuwo |