Machitidwe a Atumwi 4:2 - Buku Lopatulika2 ovutika mtima chifukwa anaphunzitsa anthuwo, nalalikira mwa Yesu kuuka kwa akufa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ovutika mtima chifukwa anaphunzitsa anthuwo, nalalikira mwa Yesu kuuka kwa akufa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Iwoŵa anali okwiya chifukwa chakuti atumwi aŵiriwo ankaphunzitsa anthu ndi kulalika kuti, “Popeza kuti Yesu adauka kwa akufa, ndiye kuti akufa adzaukanso.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iwo anakhumudwa kwambiri chifukwa atumwiwo amaphunzitsa anthu ndi kumalalikira za kuuka kwa akufa mwa Yesu. Onani mutuwo |