Machitidwe a Atumwi 3:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Petro, pompenyetsetsa iye pamodzi ndi Yohane, anati, Tiyang'ane ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Petro, pompenyetsetsa iye pamodzi ndi Yohane, anati, Tiyang'ane ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Iwo adampenyetsetsa, ndipo Petro adamuuza kuti, “Tatiyang'ana” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iwo anamuyangʼanitsitsa iye. Kenaka Petro anati, “Tiyangʼane!” Onani mutuwo |