Machitidwe a Atumwi 3:3 - Buku Lopatulika3 ameneyo, pakuona Petro ndi Yohane akuti alowe mu Kachisi, anapempha alandire chaulere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ameneyo, pakuona Petro ndi Yohane akuti alowe m'Kachisi, anapempha alandire chaulere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pamene iye adaona Petro ndi Yohane akuloŵa m'Nyumba ya Mulungu, adaŵapempha kuti ampatseko kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ataona Petro ndi Yohane ali pafupi kulowa anawapempha ndalama. Onani mutuwo |