Machitidwe a Atumwi 3:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo iye anavomereza iwo, nalingirira kuti adzalandira kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo iye anavomereza iwo, nalingirira kuti adzalandira kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Iye nkuŵayang'anadi namaganiza kuti alandira kanthu kwa iwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Munthuyo anawayangʼanitsitsa kuyembekezera kuti alandira kanthu kuchokera kwa iwo. Onani mutuwo |