Machitidwe a Atumwi 27:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo m'mene tidapita pang'onopang'ono masiku ambiri, ndi kufika movutika pandunji pa Kinido, ndipo popeza siinatilolanso mphepo, tinapita m'tseri mwa Krete, pandunji pa Salimone; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo m'mene tidapita pang'onopang'ono masiku ambiri, ndi kufika movutika pandunji pa Kinido, ndipo popeza siinatilolanso mphepo, tinapita m'tseri mwa Krete, pandunji pa Salimone; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tidayenda pang'onopang'ono pa masiku angapo, nkukafika pafupi ndi Kinido movutikira. Tsono popeza kuti mphepo idaativuta zedi, tidalephera kupitirira ulendo wathu molunjika, choncho tidadzera kumwera kwa chilumba cha Krete, titabzola Salimone. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tinayenda pangʼonopangʼono kwa masiku ambiri ndipo tinakafika kufupi ndi Knido movutikira. Pamene mphepo sinatilole kupitirira ulendo wathu molunjika, tinadzera kummwera kwa chilumba cha Krete, moyangʼanana ndi Salimoni. Onani mutuwo |