Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 27:8 - Buku Lopatulika

8 ndipo popazapazapo movutika, tinafika kumalo ena dzina lake Pokocheza Pokoma; pafupi pamenepo panali mzinda wa Lasea.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 ndipo popazapazapo movutika, tinafika kumalo ena dzina lake Pokocheza Pokoma; pafupi pamenepo panali mudzi wa Lasea.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Tidayenda movutikira m'mbali mwa chilumbacho, nkukafika ku malo ena otchedwa Madooko Okoma, pafupi ndi mzinda wa Lasea.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Timayenda movutikira mʼmbali mwa chilumbacho ndipo tinafika pa malo wotchedwa Madooko Okoma, pafupi ndi mzinda wa Laseya.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 27:8
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Yesu anati kwa ophunzira ake, Indetu ndinena kwa inu, kuti munthu mwini chuma adzalowa movutika mu Ufumu wa Kumwamba.


Ndipo popeza dooko silinakome kugonapo nyengo yachisanu, unyinji unachita uphungu ndi kuti amasule nachokepo, ngati kapena nkutheka afikire ku Fenikisi, ndi kugonako, ndilo dooko la ku Krete, loloza kumpoto ndi kumwera.


Ndipo poomba pang'ono mwera, poyesa kuti anaona chofunirako, anakoka nangula, napita m'mbali mwa Krete.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa