Machitidwe a Atumwi 27:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo kenturiyo anapezako ngalawa ya ku Aleksandriya, ilikupita ku Italiya, ndipo anatilongamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo kenturiyo anapezako ngalawa ya ku Aleksandriya, ilikupita ku Italiya, ndipo anatilongamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kumeneko mtsogoleri wa asilikali uja adapezako chombo chochokera ku Aleksandriya chimene chinkapita ku Italiya, ndipo adatikweza m'chombo chimenechi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kumeneko wolamulira asilikali 100 uja anapeza sitima ya pamadzi ya ku Alekisandriya imene imapita ku Italiya, ndipo anatikweza mʼmenemo. Onani mutuwo |