Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 26:12 - Buku Lopatulika

12 M'menemo popita ine ku Damasiko ndi ulamuliro ndi ukumu wa kwa ansembe aakulu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 M'menemo popita ine ku Damasiko ndi ulamuliro ndi ukumu wa kwa ansembe aakulu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 “Pa ulendo wina wotere, ndinkapita ku Damasiko ndi ulamuliro ndi mphamvu zondipatsa akulu a ansembe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “Pa ulendo wina wotere, ndikupita ku Damasiko ndi mphamvu ndi ulamuliro ochokera kwa akulu a ansembe,

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 26:12
12 Mawu Ofanana  

Tsoka kwa iwo amene alamulira malamulo osalungama, ndi kwa alembi olemba mphulupulu;


Ndipo panali, pamene Yeremiya anatha kunena mau onse amene Yehova anamuuza iye kuti anene kwa anthu onse, ansembe ndi aneneri ndi anthu onse anamgwira iye, ndi kuti, Udzafa ndithu.


Koma ansembe aakulu ndi Afarisi adalamula kuti, munthu wina akadziwa pokhala Iye, aulule, kuti akamgwire Iye.


Chimenenso ndinachita mu Yerusalemu: ndipo ndinatsekera ine oyera mtima ambiri m'ndende, popeza ndidalandira ulamuliro wa kwa ansembe aakulu; ndiponso pophedwa iwo, ndinavomerezapo.


dzuwa lamsana, ndinaona panjira, Mfumu, kuunika kochokera kumwamba kowalitsa koposa dzuwa kunawala pondizinga ine ndi iwo akundiperekeza.


ndipo potsiriza pake pa onse, anaoneka kwa inenso monga mtayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa