Machitidwe a Atumwi 22:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo iwo akukhala nane anaonadi kuunika, koma sanamve mau akulankhula nane. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo iwo akukhala nane anaonadi kuunika, koma sanamva mau akulankhula nane. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Anzanga apaulendo adaakuwona kuŵalako, koma mau a amene ankalankhula naneyo sadaŵamve. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Anzanga a paulendo anaona kuwalako, koma sanamve mawuwo, a Iye amene amayankhula nane. Onani mutuwo |