Machitidwe a Atumwi 22:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo ndinati, Ndidzachita chiyani, Ambuye? Ndipo Ambuye anati kwa ine, Tauka, pita ku Damasiko; kumeneko adzakufotokozera zonse zoikika kwa iwe uzichite. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo ndinati, Ndidzachita chiyani, Ambuye? Ndipo Ambuye anati kwa ine, Tauka, pita ku Damasiko; kumeneko adzakufotokozera zonse zoikika kwa iwe uzichite. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono ine ndidafunsa kuti, ‘Ndichite chiyani, Ambuye?’ Ndipo Ambuye adati. ‘Dzuka, pita ku Damasiko, kumeneko akakuuza zonse zimene Mulungu wakonza kuti ukachite.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ine ndinafunsa kuti, “Kodi ndichite chiyani Ambuye?” Ambuye anati, “Imirira ndipo pita ku Damasiko. Kumeneko adzakuwuza zonse zimene ukuyenera kuchita.” Onani mutuwo |