Machitidwe a Atumwi 11:9 - Buku Lopatulika9 Koma mau anayankha nthawi yachiwiri otuluka m'mwamba, Chimene Mulungu anachiyeretsa, usachiyesera chinthu wamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma mau anayankha nthawi yachiwiri otuluka m'mwamba, Chimene Mulungu anachiyeretsa, usachiyesera chinthu wamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma mau ochokera kumwamba aja adanenanso kachiŵiri kuti, ‘Zimene Mulungu waziyeretsa, iwe usati nzosayera.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Mawu ochokera kumwamba ananenanso kachiwiri kuti, ‘Chimene Mulungu wachiyeretsa usanene kuti ndi chodetsedwa.’ Onani mutuwo |