Machitidwe a Atumwi 11:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ndinamvanso mau akunena ndi ine, Tauka Petro; ipha, nudye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ndinamvanso mau akunena ndi ine, Tauka Petro; ipha, nudye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono ndidamva mau ondiwuza kuti, ‘Petro dzuka, ipha, udye.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka ine ndinamva mawu akuti, ‘Petro, Imirira. Ipha, nudye.’ Onani mutuwo |