Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Machitidwe a Atumwi 11:6 - Buku Lopatulika

6 chimenecho ndidachipenyetsetsa ndinachilingirira, ndipo ndinaona nyama za miyendo inai za padziko ndi zilombo, ndi zokwawa, ndi mbalame za m'mlengalenga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 chimenecho ndidachipenyetsetsa ndinachilingirira, ndipo ndinaona nyama za miyendo inai za padziko ndi zilombo, ndi zokwawa, ndi mbalame za m'mlengalenga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Nditachipenyetsetsa, ndidaonamo nyama zoŵeta ndi zakuthengo ndiponso zokwaŵa ndi mbalame zamumlengalenga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Ine ndinayangʼana mʼkati mwake ndipo ndinaona nyama za miyendo inayi za mʼdziko lapansi, zirombo, zokwawa, ndi mbalame zamlengalenga.

Onani mutuwo Koperani




Machitidwe a Atumwi 11:6
6 Mawu Ofanana  

Pamenepo anaikanso manja m'maso mwake; ndipo anapenyetsa, nachiritsidwa, naona zonse mbee.


Ndipo m'mene Iye anapinda bukulo, nalipereka kwa mnyamata, anakhala pansi; ndipo maso ao a anthu onse m'sunagogemo anamyang'anitsa Iye.


m'menemo munali nyama za miyendo inai za mitundu yonse, ndi zokwawa za padziko ndi mbalame za m'mlengalenga.


Ndinali ine m'mzinda wa Yopa ndi kupemphera; ndipo m'kukomoka ndinaona masomphenya, chotengera chilikutsika, ngati chinsalu chachikulu chogwiridwa pangodya zake zinai; ndi kutsika kumwamba, ndipo chinadza pali ine;


Ndipo ndinamvanso mau akunena ndi ine, Tauka Petro; ipha, nudye.


Ndipo Petro, pompenyetsetsa iye pamodzi ndi Yohane, anati, Tiyang'ane ife.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa