Machitidwe a Atumwi 10:6 - Buku Lopatulika6 acherezedwa iye ndi wina Simoni wofufuta zikopa, nyumba yake ili m'mbali mwa nyanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 acherezedwa iye ndi wina Simoni wofufuta zikopa, nyumba yake ili m'mbali mwa nyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Akukhala kwa Simoni wina, mmisiri wa zikopa, amene nyumba yake ili m'mbali mwa nyanja.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye akukhala ndi Simoni mmisiri wa zikopa, amene nyumba yake ili mʼmbali mwa nyanja.” Onani mutuwo |