Machitidwe a Atumwi 10:18 - Buku Lopatulika18 ndipo anaitana nafunsa ngati Simoni, wotchedwanso Petro, acherezedwako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndipo anaitana nafunsa ngati Simoni, wotchedwanso Petro, acherezedwako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adaitana nkufunsa kuti, “Kodi kuli mlendo kuno, dzina lake Simoni, wotchedwanso Petro?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iwo anayitana nafunsa ngati Simoni amene amadziwika ndi dzina loti Petro amakhala kumeneko. Onani mutuwo |