Machitidwe a Atumwi 1:18 - Buku Lopatulika18 (Uyutu tsono anadzitengera kadziko ndi mphotho ya chosalungama; ndipo anagwa chamutu, naphulika pakati, ndi matumbo ake onse anakhuthuka; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 (Uyutu tsono anadzitengera kadziko ndi mphotho ya chosalungama; ndipo anagwa chamutu, naphulika pakati, ndi matumbo ake onse anakhuthuka; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adagula munda ndi ndalama zimene adapata pochita chosalungama chija. Kumeneko adagwa chamutu, naphulika pakati, matumbo ake onse nkukhuthuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 (Yudasi anagula munda ndi ndalama zimene anazipeza pochita zoyipa zija; kumeneko, iye anagwa chamutu, naphulika pakati ndipo matumbo ake wonse anakhuthuka. Onani mutuwo |