Machitidwe a Atumwi 1:19 - Buku Lopatulika19 ndipo chinadziwika ndi onse akukhala ku Yerusalemu; kotero kuti m'manenedwe ao kadzikoka kanatchedwa Akeledama, ndiko, kadziko ka mwazi.) Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndipo chinadziwika ndi onse akukhala ku Yerusalemu; kotero kuti m'manenedwe ao kadzikoka kanatchedwa Akeledama, ndiko, kadziko ka mwazi.) Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Anthu onse okhala ku Yerusalemu adamva zimenezi, kotero kuti m'chilankhulo chao mundawo adautcha dzina loti ‘Akeledama,’ ndiye kuti, ‘Munda wa Magazi.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Aliyense mu Yerusalemu anamva zimenezi, kotero anatcha mundawo mʼchiyankhulo chawo kuti Akeledama, kutanthauza, Munda wa Magazi). Onani mutuwo |