Luka 9:62 - Buku Lopatulika62 Koma Yesu anati kwa iye, Palibe munthu wakugwira chikhasu, nayang'ana za kumbuyo, ayenera Ufumu wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201462 Koma Yesu anati kwa iye, Palibe munthu wakugwira chikhasu, nayang'ana za kumbuyo, ayenera Ufumu wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa62 Yesu adati, “Munthu amene wayambapo kulima, tsono nkumachewukiranso kumbuyo, Mulungu alibe naye ntchito mu Ufumu wake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero62 Yesu anayankha kuti, “Munthu amene akulima ndi khasu lokokedwa nʼkumayangʼana mʼmbuyo, si woyenera kugwira ntchito mu ufumu wa Mulungu.” Onani mutuwo |