Luka 9:61 - Buku Lopatulika61 Ndipo winanso anati, Ambuye ndidzakutsatani Inu; koma muyambe mwandilola kulawirana nao a kunyumba kwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201461 Ndipo winanso anati, Ambuye ndidzakutsatani Inu; koma muthange mwandilola kulawirana nao a kunyumba kwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa61 Munthu winanso adauza Yesu kuti, “Ndidzakutsatani, Ambuye, koma mundilole ndiyambe ndakatsazikana ndi anthu kunyumba.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero61 Koma winanso anati, “Ine ndidzakutsatani Ambuye; koma choyamba ndiloleni ndibwerere kuti ndikatsanzikane nalo banja langa.” Onani mutuwo |