Luka 9:31 - Buku Lopatulika31 amene anaonekera mu ulemerero, nanena za kumuka kwake kumene Iye ati adzatsiriza ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 amene anaonekera m'ulemerero, nanena za kumuka kwake kumene Iye ati adzatsiriza ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Maonekedwe ao anali aulemerero, ndipo ankakambirana za imfa ya Yesu imene ankayenera kukafera ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 anaonekera mu ulemerero opambana akuyankhulana ndi Yesu. Iwo amayankhulana za kuchoka kwake, kumene Iye anali pafupi kukakwaniritsa ku Yerusalemu. Onani mutuwo |